Neocolonial Nyasaland

This is a Draft

Poverty by Choice, a book by Donald Reuben Kamdonyo…

Madando

 1. Malawi sadzatheka
 2. Ambuye sanatisiye?
 3. Tiyambira pati?
 4. Khani ndi ndalama
 5. Ndikamaliza sukulu ndidzapanga chiyani?
 6. Anthu obwela akusokoneza zinthu
 7. Ufiti ndi kukhwima
 8. Kujoni kapena maiko ena?
 9. Magetsi akungo zima zima
 10. Ma units andithera
 11. Ndalama nchilombo
 12. Mitengo ilibe ntchito
 13. Kwacha inafooka
 14. Kodi chizungu chimativutabe?
 15. Adokodatala sakundifunira zabwino!
 16. Timangouzana sitimalemba
 17. Katangale ndi boma
 18. Umphawi sungandiletse kukhala ndi ana

Ngati sitisamala tikhala ngati abale athu aku Zambia…

Nzotheka

 1. Electricity
 2. Education
 3. Communication
 4. Currency?
 5. Leaders
 6. Mindset Change

Manyong'oments

Pa ground sipalibwino, koma omwa tea adzamwanso.


Mabvuto tho nkumati tiyambira pati? DRAFT...

By Prince Namwali, 2021-05-21